ILAYIBULALE IYA PA INTANETI
Watchtower
ILAYIBULALE IYA PA INTANETI
Chilambya
  • IBAYIBOLO
  • AMABUKU
  • INKOMANO
  • mwbr23 Novembala pp. 1-12
  • Amalifalensi Agha mu “Ubumi Bwitu Ubwachikilisitu nu Bulumbilili Akabuku aka Nkomano”

Po mwasala patali ividiyo.

Pepani, pali inyamyo yimo pakwighula ividiyo.

  • Amalifalensi Agha mu “Ubumi Bwitu Ubwachikilisitu nu Bulumbilili Akabuku aka Nkomano”
  • Amalifalensi Agha mu Ubumi Bwitu Ubwachikilisitu nu Bulumbilili Akabuku aka Nkomano—2023
  • Utumitu
  • NOVEMBALA 6-12
  • NOVEMBALA 13-19
  • NOVEMBALA 20-26
  • NOVEMBALA 27– DISEMBALA 3
  • DISEMBALA 4-10
  • DISEMBALA 11-17
  • DISEMBALA 18-24
  • DISEMBALA 25-31
Amalifalensi Agha mu Ubumi Bwitu Ubwachikilisitu nu Bulumbilili Akabuku aka Nkomano—2023
mwbr23 Novembala pp. 1-12

Amalifalensi Agha mu Ubumi Bwitu Ubwachikilisitu nu Bulumbilili Akabuku aka Nkomano

© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

NOVEMBALA 6-12

AMAZYU GHA CHALA BUKABI | JOBU 13–14

“Ka Pala Umuntu Afwa Angaba Sona nu Bumi?”

w99-CN 10/15 3 ¶1-3

Kufunafuna Kwathu Moyo Wautali

NGAKHALE lerolino ndi oŵerengeka chabe amene angatsutse malingaliro onena za kufupika kwa moyo, ngakhale kuti analembedwa zaka 3,500 zapitazo. Anthu sakukhutirabe ndi moyo wapamwamba umene amasangalala nawo kwa kanthaŵi ndipo pambuyo pake kukalamba ndi kumwalira. Choncho, njira zoyesera kutalikitsa moyo, zafala zedi m’mbiri.

M’nthaŵi ya Yobu, Aigupto ankadya mavalo anyama poyesayesa kuti mwina angabwerere ku unyamata, koma zinali zosaphula kanthu. Chimodzi mwa zolinga za sayansi ya zamankhwala ya m’nyengo zapakati, chinali kupanga mankhwala opangitsa moyo kukhala wautali. Akatswiri ambiri amene anayesayesa kutalikitsa moyo, ankakhulupirira kuti golide wopangidwa ndi anthu angapangitse moyo kukhala wosafa, ndipo kudyera m’mbale zake kungatalikitse moyo. Atao a ku China wakale ankaganiza kuti angathe kusintha makemikolo a m’thupi pogwiritsa ntchito maluso monga kusinkhasinkha, maseŵero otulutsa mpweya wambiri m’kamwa, ndi kudya pang’ono ndipo potero ankati angathe kukhala ndi moyo wosafa.

Woyendera malo wa ku Spain, Juan Ponce de León amadziŵika chifukwa cha kufunafuna kwake kasupe wa unyamata. Dokotala wina wa m’zaka za zana la 18 analangiza m’buku lake lotchedwa Hermippus Redivivus kuti anamwali ataikidwa m’kachipinda m’nyengo ya masika ndi kutengera m’mabotolo mpweya umene amapuma m’kachipindamo, ungagwiritsidwe ntchito popanga mankhwala otalikitsa moyo. N’zachionekere kuti palibe ndi imodzi yomwe mwa njira zonsezo imene inapambana.

w15-TB 4/15 32 ¶1-2

Kasi Para Khuni Ladumulika Lingasundaso?

KHUNI la cedar la ku Lebanon ndakutowa kuluska khuni la maolive. Kweni khuni la maolive likukhala vyaka vinandi. Ghanyake ghakhala vyaka pafupifupi 1,000. Misisi yake yikuthaza na kunjira chomene pasi. Para ŵadumura khuni ili, likusundaso chikuru misisi yake yindawomire.

Yobu wakamanyanga kuti nanga wangafwa, wazamuwukaso. (Job 14:​13-15) Wakayowoya vya khuni la maolive kuti walongosore fundo yakuti Chiuta wazamuwuska ŵakufwa. Yobu wakati: ‘Pali chigomezgo nanga nkhu khuni. Usange ladumulika, likuphukaso.’ Nanga kungaŵa chilangalanga, kweni para vula yalokwaso chisinga cha khuni la maolive chikusunda ‘minthavi nga ni khuni liphya.’—Job 14:​7-9.

w11-CN 3/1 22 ¶5

“Mudzalakalaka Ntchito ya Manja Anu”

Zimene Yobu ananena zikutiphunzitsa mfundo yofunika kwambiri yokhudza Yehova. Mfundo yake ndi yakuti, iye amakonda kwambiri anthu amene amamudalira ngati mmene ankachitira Yobu. Anthu amenewa amalola kuti Yehova awaumbe kukhala anthu amakhalidwe amene Mulungu amasangalala nawo. (Yesaya 64:8) Yehova amaona kuti atumiki ake okhulupirika ndi anthu amtengo wapatali kwambiri. Choncho iye ‘amalakalaka’ kuonanso anthu okhulupirika amene anamwalira. Katswiri wina wa Baibulo ananena kuti, mawu achiheberi amene palembali anawamasulira kuti ‘kulakalaka,’ “ndi amodzi mwa mawu amphamvu amene amafotokoza mmene munthu amamvera akakhala kuti akufunitsitsa chinachake.” Sikuti Yehova amangokumbukira atumiki ake, koma amalakalakanso atawaukitsa kuti akhalenso ndi moyo.

Vyo Twamanyila

it-1-E 191

Itoyi

Itoyi likimilagha ivintu vyo te vyakulondiwa pamo vyo vite ni mbombo, Abulahamu wepe akanena bunubu kwa Yehova, umwakufwanikizya akati, ‘Ne lufumbi sona nitoyi.’ (Ubwa. 18.27; ennya sona Yesa. 44.20; Jobu 30.19.) Cho chobene u Yobu akayanisya vyo abamanyani bwache bakanenagha ni ‘vyili ivya litoyi.’—Jobu 13.12.

NOVEMBALA 13-19

AMAZYU GHA CHALA BUKABI | JOBU 15–17

“Mutakabombaghe Ngati we Elifazi Pala Mukumughomya Umuntu”

w05-CN 9/15 26 ¶4-5

Pewani Maganizo Olakwika

Pa nthawi zonse zitatu zimene analankhula, Elifazi anasonyeza kuti Mulungu n’ngovuta kwambiri kum’sangalatsa moti palibe chilichonse chimene atumiki ake amachita chimene iye amasangalala nacho. Elifazi anamuuza Yobu kuti: “Taona, sakhulupirira atumiki ake; nawanenera amithenga [kapena kuti angelo] ake zopusa.” (Yobu 4:18) Kenakanso Elifazi ananena kuti Mulungu “sakhulupirira opatulika ake; ngakhale m’mwamba simuyera pamaso pake.” (Yobu 15:15) Ndipo anafunsa kuti: “Kodi Wamphamvuyonse akondwera nako kuti iwe ndiwe wolungama?” (Yobu 22:3) Bilidadi anavomerezana nawo maganizo amenewa, chifukwa nayenso anati: “Taonani, ngakhale mwezi ulibe kuwala; ndi nyenyezi siziyera pamaso [pa Mulungu].”​—Yobu 25:5.

Tiyenera kusamala kuti tisayambe kuganiza maganizo otere. Chifukwatu angatipangitse kuona kuti zimene Mulungu amafuna sizoti munthu angakwanitse. Kuganiza motere kungathe kusokoneza ubwenzi wathu weniweniwo ndi Yehova. Komanso, ngati titayamba kuganiza choncho, kodi tingathe kumvera bwinobwino malangizo enaake amene tikupatsidwa? M’malo momvera malangizowo, mtima wathu ungafike “pokwiyira Yehova weniweniyo,” motero tingakhumudwe naye. (Miyambo 19:​3, NW) Izitu zingatisokonezere kwambiri ubwenzi wathu ndi Mulungu.

w15-TB 2/15 9 ¶16

Tiŵe Ŵakujiyuyura na Ŵalusungu nga ni Yesu

16 Kayowoyero. Para tili na lusungu ‘tiyowoyenge mwakupembuzga kwa awo ŵakusuzgika maghanoghano.’ (1 Tes. 5:14) Kasi tingayowoya vichi kuti tipembuzge awo ŵakusuzgika maghanoghano? Ŵangapembuzgika chomene usange tingalongora kuti tikuŵafipira nadi mtima. Tikwenera kuŵalumba na mtima wose kuti ŵamanye ivyo ŵakuchita makora. Tiŵakumbuske kuti Yehova wali kuŵaguzira kwa mwana wake, ntheura mbakuzirwa chomene kwa iyo. (Yoh. 6:44) Tiŵasimikizgire kuti Yehova wakupwelelera ŵateŵeti ŵake awo “mbakuphyoka mu mtima,” panji awo “mbamzimu wakupera.” (Sal. 34:18) Para tikuyowoya mwalusungu ŵanyithu ŵapembuzgikenge.—Zinth. 16:24.

Vyo Twamanyila

w06-TB 3/15 14 ¶11

Fundo Zikuru za m’Buku la Job

7:​9, 10; 10:21; 16:22—Kasi ivyo vikuyowoyeka mu Malemba agha vikulongora kuti Yobu wakagomezganga yayi kuti kuzamuŵa ciwuka? Agha ni mazgu ghakuyowoya za ivyo vicitikirenge Yobu. Sono kasi wakang’anamuranga vici? Panji wakang’anamuranga kuti para wangafwa, ŵanyake ŵara ŵamuwonenge yayi. Umo iwo ŵakawoneranga, para Yobu wafwa wangaweleraso ku nyumba yake yayi nesi kumanyikwa, mpaka pa nyengo iyo Ciuta wali kuŵika. Kweniso, panji Yobu wakang’anamuranga kuti palije uyo wangafuma mu Sheole pa iyo yekha. Fundo yakuti Yobu wakagomezganga kuti ciwuka cizamuŵako yikuwoneka makora pa Job 14:​13-15.

NOVEMBALA 20-26

AMAZYU GHA CHALA BUKABI | JOBU 18–19

“Tutakabaleke bo Tukwiputa Nabo Pala Bakomana ni Ntamyo”

w22.01-TB 16 ¶9

Ivyo Tingasambirako kwa Yesu Apo Wakathiska Masozi

9 Mungakhozga awo ŵakutengera. Padera pa kulira nawo ŵena Marita na Mariya, Yesu wakaŵategherezga na kuŵakhozga. Nase tingachita mwakuyana waka na awo ŵakutengera. Dan, mulara uyo wakukhala ku Australia wakuti: “Muwoli wane wati wafwa, nkhakhumbikwiranga wovwiri. Ŵabali ŵanandi kusazgapo na ŵawoli ŵawo ŵakanitegherezganga nyengo zose. Ŵakanipanga m’pata kuti niyowoye umo nkhujipulikira, ndipo ŵakakhozgekanga soni yayi para nkhuthiska masozi. Kweniso ŵakanovwirangako ntchito zinyake, nga kusuka galimoto yane, kukagura vyakukhumbikwa, kweniso kuphika chakurya, apo chikaniŵiranga chakusuzga kuchita vinthu ivi panekha. Ndipo kanandi ŵakalombanga nane. Ŵakalongora nadi kuti mbabwezi na ŵabali awo ŵali “kubabikira kovwira mu suzgo.’”—Zinth. 17:17.

w21.09-TB 30 ¶16

Para Uyo Tikumutemwa Waleka Kuteŵetera Yehova

16 Lutilirani kovwira ŵamumbumba ŵakugomezgeka ŵa munthu uyo wasezgeka. Sono ndipo ŵakukhumbikwira chomene chitemwa chinu na kukhozgeka. (Heb. 10:​24, 25) Nyengo zinyake ŵamumbumba ya munthu uyo wasezgeka ŵangamba kuwona kuti ŵanyake mu mpingo ŵaleka kuchezga nawo nga umo ŵakachitiranga pambere mubali wawo wandasezgeke. Tingazomerezganga yayi kuti vyanthena ivi vichitike. Ŵawukirano awo ŵapapi ŵawo ŵali kuwuleka unenesko ndiwo ŵakukhumbikwira chomene kuŵakhozga na kuŵawonga pa ivyo ŵakuchita. Maria, uyo mfumu wake wakasezgeka na kuyileka mbumba yake, wakuti: “Ŵabwezi ŵane ŵanyake ŵakizanga kunyumba kwane na kuniphikira chakurya kweniso kunovwira kusambira Baibolo na ŵana ŵane. Nawo vikaŵaŵinya ndipo ŵakalira nane. Ŵakanivikiliranga para ŵanthu ŵakuthandazga nkhani zautesi zakukhwaskana na ine. Ŵakanikhozga chomene!”—Rom. 12:​13, 15.

w90-CN 9/1 22 ¶20

Kodi Mukukalimira?

20 Bungwe la akulu liyenera kuzindikira kuti kuchotsedwa pakukhala mkulu kungachititse kupsinjika maganizo kwa amene anali woyang’anira kapena mtumiki wotumikira, ngakhale ngati angatule mwaŵi umenewo modzifunira. Ngati sanachotsedwe mumpingo, ndipo akulu akuwona kuti mbaleyo ali wokhwethemulidwa maganizo, iwo ayenera kupereka thandizo lachikondi lauzimu. (1 Atesalonika 5:14) Iwo ayenera kumthandiza kuzindikira kuti ali wofunika mumpingo. Ngakhale ngati uphungu wakhala wofunikira, sikungatenge nthaŵi yaitali kuti munthu wodzichepetsa ndi woyamikira alandirenso mwaŵi wowonjezereka wakutumikira mumpingomo.

Vyo Twamanyila

w94-CN 10/1 32

Mphamvu ya Mawu Achifundo

Komabe, pamene Yobu mwiniyo anafunikira chilimbikitso, Elifazi ndi anzake sananene mawu achifundo. Anaimba mlandu Yobu chifukwa cha tsoka lake, akumasonyeza kuti ayenera kukhala atachita tchimo la mseri. (Yobu 4:8) The Interpreter’s Bible imati: “Chimene Yobu afunikira ndicho chifundo cha mtima wa munthu. Chimene alandira ndicho mpambo wa mawu achipembedzo ojeda ndi ndemanga za makhalidwe zimene zili ‘zoona’ ndi zabwinodi.” Yobu anavutika kwambiri atamva zokamba za Elifazi ndi anzake kwakuti anakakamizika kulira kuti: “Mudzasautsa moyo wanga kufikira liti, ndi kundithyolathyola nawo mawu?”—Yobu 19:2.

Tisachititse konse mtumiki mnzathu wa Mulungu kulira mosautsidwa mtima chifukwa cha mawu athu opanda nzeru ndi opanda chifundo. (Yerekezerani ndi Deuteronomo 24:15.) Mwambi wa Baibulo umachenjeza kuti: “Zimene mumalankhula zingapulumutse moyo kapena kuuwononga; chotero muyenera kulandira zotsatirapo za mawu anu.”—Miyambo 18:​21, TEV.

NOVEMBALA 27– DISEMBALA 3

AMAZYU GHA CHALA BUKABI | JOBU 20–21

“Ubugholosu Tutangabufwanikizya ni Chuma”

w07-CN 8/1 29 ¶12

Kodi Ndinu “Wolemera kwa Mulungu”?

12 Yesu anasiyanitsa kukhala wolemera kwa Mulungu ndi kudzikundikira chuma chakuthupi. Choncho, Yesu ankatanthauza kuti cholinga chathu chachikulu pamoyo chisakhale kudzikundikira chuma chakuthupi n’kumasangalala nacho. M’malo mwake, tiyenera kugwiritsira ntchito chuma chathucho polimbikitsa ubwenzi wathu ndi Yehova. Kuchita zimenezi kudzatithandiza kukhala olemera kwa Mulungu. Chifukwa chiyani? Chifukwa chakuti iye amatidalitsa kwambiri tikamatero. Baibulo limati: “Madalitso a Yehova alemeretsa, sawonjezerapo chisoni.”—Miyambo 10:22.

Vyo Twamanyila

w95-CN 1/1 9 ¶19

Kumlaka Satana ndi Ntchito Zake

19 Tifunikira kudziŵa kuti Yobu mtumiki wa Mulungu analimbana ndi “zolingirira” zimene Satana anapereka kupyolera mwa Elifazi ndi Zofari. (Yobu 4:​13-18; 20:​2, 3) Chotero Yobu anavutika ndi “chisoni,” chikumambwetukitsa ‘mawu osokera’ a “zowopsa” zosautsa maganizo ake. (Yobu 6:​2-4; 30:​15, 16) Elihu anamvetsera kwa Yobu mwakachetechete namthandizadi kuona njira ya yanzeru kwambiri imene Yehova amaoneramo zinthu. Mofananamo lerolino, akulu achifundo amasonyeza kuti amasamala ovutika mwa kusawonjezera ‘zosenza’ pa anthu otero. M’malo mwake, monga Elihu, iwo moleza mtima amamvetsera kwa iwo ndiyeno amagwiritsira ntchito mafuta otontholetsa a m’Mawu a Mulungu. (Yobu 33:​1-3, 7; Yakobo 5:​13-15) Chotero aliyense amene malingaliro ake akuvutika ndi zopsinja maganizo, zenizeni kapena zongolingalira, kapena amene ‘akuwopsezedwa ndi maloto, . . . ndi masomphenya’ monga Yobu, angapeze chitonthozo cha m’Malemba mumpingo.—Yobu 7:14; Yakobo 4:7.

DISEMBALA 4-10

AMAZYU GHA CHALA BUKABI | JOBU 22–24

“Ka Umuntu Angaba Wakulondiwa kwa Chala?”

w05-CN 9/15 27 ¶1-3

Pewani Maganizo Olakwika

Maganizo akuti Mulungu n’ngovuta kum’sangalatsa amayendera limodzi ndi maganizo akuti Mulungu saona anthu ngati kanthu. Panthawi yachitatu imene Elifazi analankhula ananenapo mawu akuti: “Kodi munthu apindulira Mulungu? Koma wanzeru angodzipindulira yekha.” (Yobu 22:2) Apatu Elifazi anali kutanthauza kuti munthu sanunkha kanthu kwa Mulungu. Bilidadi anakhudzaponso mfundo yomweyi ponena kuti: “Munthu akhala bwanji wolungama kwa Mulungu? Kapena wobadwa ndi mkazi akhala woyera bwanji?” (Yobu 25:4) Tikatengera maganizo amenewa, tingafunse kuti kodi Yobu poti anali munthu, ankadzivutitsiranji kuganiza kuti angathe kukhala wolungama pamaso pa Mulungu?

Anthu ena masiku ano amavutika ndi maganizo olakwika okhudza moyo wawo. N’kutheka kuti amaganiza choncho chifukwa cha mmene analeredwera, mavuto amene akumana nawo pa moyo wawo, mwinanso kusankhidwa mtundu kapena fuko. Koma Satana ndi ziwanda zake amasangalalanso kwambiri kuvutitsa anthu. Amadziwa kuti akangochititsa munthu kuyamba kumva kuti palibe chimene angachite choti Mulungu Wamphamvuyonse n’kusangalala nacho, m’posavuta kuti munthuyo asowe kolowera. Kenaka mwapang’onopang’ono munthuyo angathe kuyamba kutalikirana ndi Mulungu wamoyo mwinanso kufika polekana naye kumene.—Ahebri 2:1; 3:12.

Kukalamba ndiponso matenda amatilepheretsa kuchita zinthu zina. Tingaone kuti tikulephera kuchita zambiri mu utumiki wa Ufumu poyerekezera ndi zimene tinkachita tili aang’ono, tili athanzi, ndiponso tili amphamvu. M’pofunika kwambiri kuzindikira kuti Satana ndi ziwanda zake amafuna kuti tiziganiza kuti zimene tikuchita panopa si zoti Mulungu n’kusangalala nazo ayi. Tiyeni tiyesetse kupewa maganizo oterewa.

w95-CN 2/15 27 ¶6

Phunziro pa Kusamalira Mavuto

Mabwenzi ake atatuwo anadetsanso mtima wa Yobu mwa kunena za malingaliro a iwo eni m’malo mwa nzeru yaumulungu. Elifazi anafikiradi pakunena kuti ‘Mulungu sakhulupirira atumiki ake’ ndi kuti zinalibe kanthu kwa Yehova kuti kaya Yobu anali wolungama kapena ayi. (Yobu 4:18; 22:​2, 3) Nkovuta kulingalira za mawu ena olefula maganizo kwambiri​—kapena onama kwambiri​—kuposa amenewo! Mosadabwitsa, Yehova pambuyo pake anadzudzula Elifazi ndi mabwenzi ake kaamba ka mwano umenewu. “Simunandinenera choyenera,” iye anatero. (Yobu 42:7) Koma chinenezo china chovulaza koposa chinalinkudza.

w03-CN 4/15 14-15 ¶10-12

Achinyamata Amene Amakondweretsa Mtima wa Yehova

10 Monga mmene zikuonekera m’nkhani ya m’Baibulo imeneyi, Satana anakayikira osati kukhulupirika kwa Yobu yekha komanso kwa ena onse amene amatumikira Mulungu, kuphatikizapo inuyo. Ndipotu, pofotokoza za anthu onse, Satana anauza Yehova kuti: “Khungu kulipa khungu, inde munthu [osati Yobu yekha koma aliyense] adzapereka zonse ali nazo kuombola moyo wake.” (Yobu 2:4) Kodi mukuona mbali yanu pankhani yofunika kwambiri imeneyi? Monga mmene lemba la Miyambo 27:11 lasonyezera, Yehova akunena kuti pali chinachake chimene mungapereke kwa iye, chimene chingathandize kuti amuyankhe nacho wotonzayo, Satana. Tangoganizani! Wolamulira wa Chilengedwe Chonse akukupemphani kuthandiza nawo poyankha nkhani yaikulu kwambiri kuposa ina iliyonse. Inde, muli ndi udindo ndiponso mwayi waukulu. Kodi mungachite zimene Yehova akukupemphani? Yobu anatero. (Yobu 2:​9, 10) Yesu anateronso pamodzi ndi anthu ena ambirimbiri kuyambira kale mpaka pano, kuphatikizapo achinyamata ambiri. (Afilipi 2:8; Chivumbulutso 6:9) Inunso mungachite chimodzimodzi. Komabe, dziŵani kuti n’zosatheka kukhala opanda mbali pankhani imeneyi. Mwa zochita zanu, mudzasonyeza kuti muli ku mbali yotonza ya Satana kapena kumbali ya yankho la Yehova. Kodi mudzasankha kukhala mbali iti?

Yehova Amakusamalirani

11 Kodi zimene mwasankha kuchita zimakhudza Yehova? Kodi anthu okwanira sanasonyeze kale kukhulupirika zimene zingamuthandize kumuyankha mokwanira Satana? N’zoona kuti Mdyerekezi ananena kuti palibe amene amatumikira Yehova chifukwa chomukonda, kuneneza kumene kwatsimikiziridwa kale kuti kunali kwabodza. Komabe, Yehova akufuna kuti inuyo mukhale ku mbali yake pankhani ya ulamuliroyi chifukwa amakusamalirani monga munthu panokha. Yesu anati: “Sichili chifuniro cha Atate wanu wa kumwamba kuti mmodzi wa aang’ono awa atayike.”—Mateyu 18:14.

12 Inde, Yehova amaona zimene mwasankha kuchita. Kuposanso pamenepo, zimene mwasankhazo zimamukhudza. Baibulo limafotokoza momveka bwino kuti zinthu zabwino kapena zoipa zimene anthu amachita zimamukhudza kwambiri. Mwachitsanzo, pamene Aisrayeli anapanduka mobwerezabwereza, “zinam’pweteka” Yehova. (Salmo 78:​40, 41, NW) Chigumula cha m’nthaŵi ya Nowa chisanachitike, pamene “kuipa kwa anthu kunali kwakukulu,” Yehova “anavutika m’mtima mwake.” (Genesis 6:​5, 6) Taganizirani tanthauzo la zimenezi. Ngati mungasankhe kuchita zinthu zoipa, mudzachititsa Mlengi wanu kupwetekedwa. Zimenezi sizikutanthauza kuti Mulungu ndi wofooka kapena kutengeka maganizo kumamulamulira ayi. M’malo mwake, iye amakukondani ndipo amasamala za moyo wanu. Koma ngati muchita zabwino, mtima wa Yehova umakondwera. Amasangalala osati kokha chifukwa chakuti wapeza yankho lina kwa Satana komanso chifukwa chakuti tsopano angakhale Wokubwezerani Mphoto. Ndipo iye amafuna kuchita zimenezi. (Ahebri 11:6) Inde, Yehova Mulungu ndi Atate wanu wachikondi.

Vyo Twamanyila

w04-CN 7/15 21-22

Fiskani Vilato Vinu Vyauzimu Kuti Muchindike Mlengi Winu

Ghanaghanirani waka umo Yehova wakalengera vinthu. Yehova wakayowoya waka mazgu ndipo “kukaŵa mise ndiposo kukaŵa mulenji,” ndipo wakaŵika mphaka pakati pa usiku na mhanya. (Genizesi 1:​5, 8, 13, 19, 23, 31) Kufuma waka pakwamba, Yehova wakamanyanga makora chilato icho wakapangiranga chinthu chilichose. Ndipo Chiuta wakafiska chilato chake pakulenga vinthu. (Chivumbuzi 4:11) Yobu wakalemba kuti “para [Yehova] wakukhumba kuchita chinthu, wakuchita.” (Yobu 23:13) Yehova wakwenera wakakhorwa kuwona “vyose ivyo wakapanga” ndipo wakati “vikaŵa viwemi chomene”!—Genizesi 1:31.

Kuti tifiske vilato vinthu, nase tikwenera kuŵikapo mtima chomene. Kasi ntchivichi chingatovwira kuti tifiske vilato vithu? Nanga ni apo charu chikaŵa chawaka, chambura kanthu, Yehova wakaghanaghaniranga umo charu chizamuwonekera para wamara kuchilenga, ivi vikamupanga uchindami na ntchindi. Nase tingafiska makora vilato vithu para tikughanaghanira chomene pa viwemi ivyo tizamusanga. Ivi ndivyo vikachitikira munyamata munyake wa vyaka 19 zina lake Tony. Iyo wakaluwa yayi umo wakakondwera wakati wawona ofesi ya munthavi ya Ŵakaboni ŵa Yehova iyo yili ku Western Europe. Kufuma waka nyengo yira Tony wakajifumbanga kuti, ‘Kasi umoyo ungaŵa uli usange ningakhala na kuteŵetera ku malo agha?’ Tony wakaleka yayi kughanaghanirapo ndipo wakaŵikapo mtima kuti mpaka wakateŵetereko. Pakati pajumpha vyaka 7 wakachemeka kukateŵetera pa ofesi iyi, ndipo wakakondwa chomene!

DISEMBALA 11-17

AMAZYU GHA CHALA BUKABI | JOBU 25-27

“Ukusubaliwa Kutakulondiwa Ukuti TubeTasi Swe Bakufikapo”

it-1-E 1210 ¶4

Ukusubaliwa

Yobu. U Yobu, akabako mukabalilo ko u Josefu akafwila ukufika mukabalilo ka Mozesi. Ibayibolo likumulingannya ukuti umwene akaba ‘wakugholoka sona musubaliwa [Heb., tam], akamoghopagha u Chala nu kubenga vivyo vibibi.’ (Jobu 1.1; ennya YOBU.) Amalalusyo gho u Chala akamulalusyo u Satana aghakukwafyannya nu Yobu akabalilo ko abantumi bakakomana kumwanya ghakulangizya ukuti inkani yo pakasi pa u Yehova u Chala nu Satana yikonganyapo vyo swe bantu tukubomba ukuti tulangizye ukuti swe basuliwa. U satana akokongelezya ukunena ukuti u Yobu akumwiputa u Chala ichifukwa cha bulili sona ukuti aghepo amapindu. Apa vikulangizya ukuti u Satana akakayikilagha waghe u Yobu mu subaliwa kwa Chala. U Chala akitikizya ukuti u Satana apoke u katundu uwa yobu poka na bana ba bache loli u Satana akapotwa ukunanga ubusubaliwa bwa Yobu. (Jobu 1.6–2.3) Pisinda pache, u Satana akandasona ukumulonga u Yobu ukuti mulili sona akakwanisya ukuba mu subaliwa pakabalilo aka ichifukwa intamyo yo akakomana nayo yitakakwafya umubili wache loli akataya bulo ukatundu na bana. (Jobu 2.4, 5) Pabumalilo u Satana akamubinika u Yobu ni mbina iya kubaba akapangisya ukuti umuchi wache amupe ubulongozi ububibi, Sona akapangisya abamanyani bache bo batakonkagha ifundo zya Chala ukuti bamunyozaghe. (Jobu 2.6-13; 22.1, 5-11) Loli u Yobu akanena ukuti inti abukilile ukuba musubaliwa kwa chala akanena ukuti: ‘Nkwiza ukubukilila ukuba musubaliwa mpaka po nkwiza pa kufwila Inti nize imbulemasye ubugholosu sona te nize imbutayepo; umoyo wane te wunsusyepo akabalilo kosi ko inti imbe nu bumi.’ (Jobu 27.5, 6) Pakuti u Yobu akabukilila ukuba musubaliwa vikalangizya ukuti umulwani wa Chala akaba mu myasi.

w19.02-TB 3 ¶3-5

Sungilirani Kunyoloka Kwinu!

3 Kwa ise ŵateŵeti ŵa Chiuta, kunyoloka chikung’anamura kutemwa Yehova na mtima wose na kujipeleka kwa iyo na kudangizga khumbo lake pa chilichose icho tikuchita. Wonani umo lizgu lakuti kunyoloka likugwiliskikira ntchito mu Baibolo. Mu Baibolo, lizgu Lachihebere ilo lili kung’anamulika kuti “kunyoloka” ni: chinthu chamsuma, chambura kupeleŵera, panji chambura kalema. Mwachiyelezgero, Ŵaisrayeli ŵakapelekanga sembe za nyama kwa Yehova, ndipo Dango likatenge nyama izi zikeneranga kuŵa zambura kalema.b (Lev. 22:​21, 22) Ŵanthu ŵa Chiuta ŵakazomerezgekanga yayi kupeleka nyama ya kalundi kamoza, khutu, panji jiso limoza; kweniso ŵakeneranga yayi kupeleka yilwari. Chakuzirwa chomene kwa Yehova chikaŵa kuti nyama yiŵenge yambura kalema, yamsuma, panji yambura kupeleŵera. (Mal. 1:​6-9) Tingapulikiska chifukwa icho Yehova wakakhumbiranga nyama yamsuma panji yambura kalema. Para tagura chinthu chinyake, kwali ntchipambi, buku, panji chiteŵetero chinyake, tingakhumba yayi kuti chinthu icho chiŵe chakudolokadoloka, chakutchejeka panji icho chilije vigaŵa vinyake. Tingakhumba kuti chinthu icho chiŵe chamsuma, chambura kalema, panji chambura kupeleŵera. Yehova nayo wakukhumba kuti tigomezgekenge kwa iyo na kumutemwa na mtima wose. Kugomezgeka na chitemwa chithu vikwenera kuŵa vyamsuma, vyambura kalema, panji vyambura kupeleŵera.

4 Kasi tikwenera kuŵa ŵakufikapo kuti tiŵe ŵakunyoloka? Nyengo zinandi tikubudiska, ndipo tikujipulika kuti ndise ŵakupeleŵera. Wonani vifukwa viŵiri ivyo vingatovwira kumanya kuti tikwenera kuŵa dankha ŵakufikapo yayi kuti tiŵe ŵakunyoloka. Chakwamba ntchakuti Yehova wakuŵika chomene mahara pa maubudi ghithu yayi. Mazgu ghake ghakutiphalira kuti: “Imwe Ya, muŵenge kuti mukuŵanika maubudi, kasi ni njani wangima, A Yehova?” (Sal. 130:3) Wakumanya kuti ndise ŵambura kufikapo, ŵakwananga, ndipo wakutigowokera na mtima wose. (Sal. 86:5) Chachiŵiri ntchakuti Yehova wakumanya ivyo tingafiska na ivyo tingatondeka, ndipo wakukhazga vinandi yayi kufuma kwa ise kuluska ivyo tingafiska. (Ŵazgani Salimo 103:​12-14.) Kasi tingaŵa wuli ŵamsuma, ŵambura kalema, panji ŵambura kupeleŵera mu maso gha Yehova?

5 Kuti ŵateŵeti ŵa Yehova ŵaŵe ŵakunyoloka, ŵakwenera kuŵa na chitemwa. Chitemwa chithu kwa Chiuta na kujipeleka na mtima wose kwa Adada ŵithu ŵakuchanya, vikwenera kulutilira kuŵa vyamsuma, vyambura kalema, panji vyambura kupeleŵera. Para chitemwa chithu chikulutilira kuŵa nthena nanga tingayezgeka, mbwenu tili ŵakunyoloka. (1 Mid. 28:9; Mat. 22:37) Ghanaghaniraniso za Ŵakaboni ŵatatu awo ŵalongosoreka pakwambilira. Chifukwa wuli ŵakagomezgeka? Kasi msungwana wakakhumbanga yayi kukondwa pa sukulu, panji kasi munyamata wakakhumbanga kukhozgeka soni apo wakapharazganga nyumba na nyumba, panji kasi mwanalume wa banja yura wakakhumbanga kulekeskeka ntchito? Napachoko pose. M’malo mwake, ŵakamanyanga kuti Yehova wali na fundo zaurunji, ndipo maghanoghano ghawo ghakaŵa pakukondweska Adada ŵawo ŵakuchanya. Chitemwa icho ŵakaŵa nacho pa iyo ndicho chikaŵatuma kuti ŵadangizge vyakukhumba vyake. Ndipo ŵakalongora kuti ŵakaŵa ŵakunyoloka.

Vyo Twamanyila

w16.11-TB 9 ¶3

Baibolo Likutovwira Kuteŵetera Yehova Mwakukolerana

3 Vinthu ivyo Yehova wali kulenga vikulongora kuti iyo ni Chiuta wandondomeko kuluska waliyose. Baibolo likuti: “Yehova wali kujintha charu chapasi mu vinjeru. Wali kukhozga machanya mu umanyi.” (Zinth. 3:19) Ise tikumanya waka ‘tuvigaŵa tuchoko waka twa nthowa za Chiuta’ ndipo “tikupulika waka kuphwepwerezga kwake!” (Yobu 26:14) Kweni vinthu vichoko waka ivyo tikumanya vyakukhwaskana na mapulaneti, nyenyezi, kweniso vipingausiku, vikutovwira kugomezga kuti Yehova wali kuviŵika nadi vinthu mu ndondomeko yiwemi. (Sal. 8:​3, 4) Vipingausiku vili na nyenyezi mamiliyoni ghanandi chomene, ndipo vyose vikwenda mu ndondomeko kuyana na umo Yehova wali kuvipangira. Mapulaneti ghose ghakwenda makora mu ndondomeko yake pakuzingilira zuŵa, ndipo ghakwenda nga kuti nagho ghali kupika malango gha pa msewu. Kuyowoya unenesko umo vinthu ivi vikwendera mu ndondomeko, vikutovwira kumanya kuti Yehova, uyo wali “kulenga kuchanya mwaluso” na charu chapasi, ndiyo tikwenera kumulumba na kumusopa.—Sal. 136:​1, 5-9.

DISEMBALA 18-24

AMAZYU GHA CHALA BUKABI | JOBU 28-29

“Ka Muli ni Nkalo Inyiza Ngati we Yobu?”

w02-TB 5/15 22 ¶19

Citirani Lusungu Awo Ŵali mu Suzgo

19 Nkani izo tadumbiskana mu Baibolo zikukhozgera fundo yakuti tikwenera kucitira lusungu awo ŵakukhumba covwiro ico pa iwo ŵekha ŵangakwaniska yayi. Fuko la Abrahamu kuti lirutilire, Betuel wakenera kukolerana nayo. Thupi la Yakobe kuti lisungike mu Kenan, Yosefe wakenera kumovwira. Kuti wababe muhariri wa Naomi, Ruth wakenera kumovwira Naomi. Kwambura covwiro, Abrahamu, Yakobe, na Naomi ŵakatenge ŵakwaniskenge cara ivyo ŵakakhumbanga. Mwakuyana waka, nase tikwenera kucitira lusungu comene-comene awo ŵali mu suzgo. (Zintharika 19:17) Tiyeni tirondezge sekuru wakale Job, uyo wakapwerereranga ‘mukavu uyo wakaliranga, na muranda uyo wakaŵavye wakumovwira’ na “uyo wakaŵa pafupi kuparanyika.” Job ‘wakacitiskaso mtima wa cokoro kwimba na cimwemwe’ ndipo wakaŵaso “maso ku ŵacibulumutira na marundi ku ŵagonti.”—Job 29:​12-15.

it-1-E 655 ¶10

Imyenda

Akabalilo kamo Ibayibolo lingalingannya pamo ukulongosola ichintu chimo pakubombezya imyenda. Iyunifomu pamo ichakuvwala chimo chingalangizya igulu pamo imbali yimo yo umuntu ali. Umwakuyana bulo Ibayibolo lingalingannya ivyakuvwala ukuti lilongosole amalo pamo ichigaba cho umuntu ali sona imbombo yo umuntu akubomba. U Yesu akabomba bunubu pakulingannya ichifwanikizyo icha myenda iya sendwa. (Mata. 22.11, 12; enya HEADDRESS; SANDAL.) Pa Ubuvumbuli 16.14, 15, pakunena ukuti Umwene u Yesu Kilisitu akasoka ukuti mutakaghonaghe mwabuzimu sona mutakavulaghe inkalo zyo zikubamanyisya ukuti mwe bakaboni abasubaliwa aba Chala uwa bwanaloli. Ili likwiza ukuba lisiku ilya koghofya ilya “inkondo pisiku ilikulu ilya Chala Uwamakaghosi.”

w09-CN 2/1 15 ¶3-4

Mayina Atanthauzo?

Sitingasankhe tokha dzina limene timapatsidwa pobadwa. Komabe, timapanga tokha mbiri imene timakhala nayo. (Miyambo 20:11) Bwanji osadzifunsa kuti: ‘Ngati Yesu kapena atumwi ake akanakhala ndi mwayi wondipatsa dzina, kodi akanandipatsa lotani? Kodi dzina labwino lofotokoza mbiri yanga kapena khalidwe langa lingakhale liti?

Funso limeneli tifunika kuliganizira mofatsa kwambiri. N’chifukwa chiyani tikutero? Mfumu yanzeru Solomo inalemba kuti: “Mbiri yabwino ifunika kopambana chuma chambiri.” (Miyambo 22:1) Ndithudi, ngati tili ndi dzina labwino kapena mbiri yabwino m’dera limene timakhala, ndiye kuti tili ndi chuma chamtengo wapatali. Koma chofunika kwambiri n’chakuti tikakhala ndi dzina labwino ndi Mulungu ndiye kuti tidzapeza chuma chosatha. Kodi zimenezi zingachitike motani? Mulungu akulonjeza kuti adzalemba mu “buku la chikumbutso” mayina a anthu amene amamuopa ndipo adzawapatsa moyo wosatha.​—Malaki 3:16; Chivumbulutso 3:5; 20:​12-15.

Vyo Twamanyila

g00-CN 7/8 29 ¶3

Mwetulirani—N’zothandiza kwa Inu!

Kodi kumwetulira kumasinthadi zinthu? Chabwino, kodi mukukumbukira nthaŵi yomwe kumwetulira kwa munthu winawake kunakupatsani mpumulo kapena kunakukhalitsani womasuka? Kapena pamene munachita mantha kapena kudzimva kukhala wokanidwa chifukwa chakuti winawake sanakumwetulireni? Inde, kumwetulira kumasinthadi zinthu. Kumakhudza onse aŵiri, womwetulirayo komanso womwetuliridwa. Ponena za adani ake, munthu wa m’Baibulo Yobu anati: “Ndinawaseka akapanda kulimbika mtima; ndipo sanagwetsa kusangalala kwa nkhope yanga.” (Yobu 29:24) “Kusangalala” kwa nkhope ya Yobu kuyenera kuti kunasonyeza chimwemwe chake kapena kukondwera kwake.

DISEMBALA 25-31

AMAZYU GHA CHALA BUKABI | JOBU 30–31

“Ka u Yobu Akabukilila Buli-Buli Ukuba Muzelu”

w10-TB 4/15 21 ¶8

Lekani Kulaŵiska Vinthu Vyawakawaka

8 Ŵakhristu ŵaunenesko nawo ŵakusuzgika na makhumbiro gha maso na gha thupi. Lekani pakuyowoya za vinthu ivyo tikuwona na kudokera, Mazgu gha Ciuta ghakuticiska kuti tiŵe ŵakujikora. (1 Kor. 9:​25, 27; ŵazgani 1 Yohane 2:​15-17.) Munthu wakunyoloka Yobu, wakamanyanga kuti pali kukolerana kukuru pakati pa kuwona na kudokera. Iyo wakati: “Ndacita phangano na maso ghane; ine ndingamanya uli kulaŵiska mwali?” (Job 31:1) Yobu wakakana waka kukora mwanakazi na cilato ciheni yayi, wakakana nanga nkhuŵa na maghanoghano ghantheura. Yesu wakati maghanoghano ghithu ghaleke kubinkhiskika na vinthu viheni. Iyo wakati: “Waliyose uyo wakulutilira kulaŵiska mwanakazi na kuŵa nayo na khumbiro, wacita nayo kale uleŵi mu mtima wake.”—Mat. 5:28.

w08-CN 9/1 11 ¶4

Tsatirani Zikwangwani

Musanalowe m’njira imeneyi, dzifunseni kuti, ‘Kodi njira iyi ikupita kuti?’ Kuyamba mwaganizira kaye pang’ono za “chitsiriziro chake” kungakuthandizeni kupewa kuchita zinthu zimene zingakulowetseni m’mavuto. Njira yonse ya anthu amene amanyalanyaza zikwangwani zoterezi ndi yodzaza ndi mavuto monga Edzi, matenda osiyanasiyana opatsirana pogonana, kutenga mimba zapathengo, kutaya mimba, kutha kwa mabanja, kapena kudana ndi anthu ena ndiponso kuvutika ndi chikumbumtima. Mtumwi Paulo anafotokoza momveka bwino za mapeto a njira ya anthu amene amachita zachiwerewere. Iye anati “sadzalowa mu ufumu wa Mulungu.”​—1 Akorinto 6:​9, 10.

w10-TB 11/15 5-6 ¶15-16

Ŵawukirano, Longozgekani na Mazgu gha Ciuta

15 Mphawuli apo mukuwona kuti mungayezgeka comene kuti munangire Ciuta, para muli na ŵanyinu, panji para muli kwamwekha? Para muli ku sukulu panji ku nchito mukwenera kuti mukuŵa maso comene mwauzimu kuti muleke kucita cinthu ico cingatimbanizga ubwezi winu na Ciuta. Kweni para mwafwasa kwamwekha ndipo mungayezgeka comene kuti mucite vinthu vyambura kukondweska Ciuta.

16 Cifukwa wuli mukwenera kupulikira Yehova nanga ni para muli kwamwekha? Kumbukani kuti para mwacita viheni mukukwenyerezga Yehova, kweni para mwacita viwemi mukukondweska mtima wake. (Gen. 6:​5, 6; Zinth. 27:11) Yehova wakukhwaskika na ivyo mukucita cifukwa “wakumupwelelerani.” (1 Pet. 5:7) Wakukhumba kuti mumupulikirenge mwakuti musange candulo. (Yes. 48:​17, 18) Mu nyengo ya Ŵaisrayeli, cikamuŵinyanga comene para ŵateŵeti ŵake ŵanyake ŵamugalukira. (Sal. 78:​40, 41) Nangauli ŵanji ŵakacitanga nthena, kweni Yehova wakamutemwa comene Daniyeli, mwakuti mungelo wakati ni “munthu wakutemweka.” (Dan. 10:11) Cifukwa wuli? Daniyeli wakagomezgekanga kwa Ciuta para wali pa wumba kweniso para wali kwayekha.—Ŵazgani Daniel 6:10

Vyo Twamanyila

w05-TB 11/15 11 ¶3

Luso Lomvetsera Ena Mwachikondi

Anzake a mwamuna uja Yobu anamvetsera nkhani zosachepera 10 kuchokera kwa Yobu. Komabe, Yobu ananena kuti: “Ha! ndikadakhala naye wina wakundimvera.” (Yobu 31:35) N’chifukwa chiyani Yobu analankhula choncho? Chifukwa chakuti kumvetsera kwawo sikunali kotonthoza. Sanasamale za iye ndipo sanafune kumvetsa maganizo ake. N’zoona kuti iwo sizinawakhudze mtima ngati mmene zimakhalira ndi anthu achifundo. Koma mtumwi Petro anapereka uphungu wakuti: “Khalani nonse a mtima umodzi, ochitirana chifundo, okondana ndi abale, achisoni, odzichepetsa.” (1 Petro 3:8) Kodi tingasonyeze bwanji chifundo? Njira imodzi ndiyo kukhudzidwa ndi maganizo a wina ndi kuyesa kuwamvetsetsa. Kupereka ndemanga zotonthoza ndi njira imodzi yosonyezera kuti zikutikhudza. Mwachitsanzo tinganene kuti, “zimenezo n’zokhumudwitsadi,” kapena kuti “koma ndiye anakumva molakwikatu.” Njira ina ndiyo kulankhula zomwe munthu akutiuzazo m’mawu athuathu, ndipo zimenezi zimasonyeza kuti tikumvetsa zimene munthuyo akunena. Kumvetsera mwachikondi kumatanthauza kumva mosamala osati mawu okha ayi, koma ngakhalenso kuzindikira zimene munthuyo akuganiza ngakhale sanazilankhule.

    Amabuku gha mu Lambya (2012-2025)
    Fuma
    Ingila
    • Chilambya
    • Tuma
    • Vyo Mukulonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Indaghilo
    • Ukusunga Ichisisi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Ingila
    Tuma