Levitiko 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake. Salimo 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa,+Kuti dzina lawo lisatchulidwenso padziko lapansi.+ Ezekieli 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndidzamuyang’ana mokwiya+ n’kumuika kuti akhale chenjezo+ ndi mwambi.+ Ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu anga,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’+
10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.
16 Nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa,+Kuti dzina lawo lisatchulidwenso padziko lapansi.+
8 Ine ndidzamuyang’ana mokwiya+ n’kumuika kuti akhale chenjezo+ ndi mwambi.+ Ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu anga,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’+