-
Genesis 19:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Chonde, taonani pali tauni yaingʼono pafupipa ndipo ndingathe kuthawira kumeneko. Tauni imeneyi ndi yaingʼono. Chonde ndiloleni ndithawire mʼtauni imeneyi. Ndikatero, ndipulumutsa moyo wanga.”
-