Mika 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yakobo mudzamusonyeza kukhulupirika.Abulahamu mudzamusonyeza chikondi chokhulupirika,Ngati mmene munalumbirira kwa makolo athu kalekale.+ Luka 1:72, 73 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Adzakwaniritsa zimene analonjeza makolo athu akale ndipo adzawasonyeza chifundo. Iye adzakumbukira pangano lake loyera,+ 73 lumbiro limene analumbira kwa kholo lathu Abulahamu,+ Aheberi 6:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu, analumbira pa dzina lake chifukwa panalibe wina wamkulu kuposa iyeyo amene akanamulumbirira.+ 14 Iye anati: “Ndithudi ndidzakudalitsa ndipo ndidzachulukitsa mbadwa zako.”+
20 Yakobo mudzamusonyeza kukhulupirika.Abulahamu mudzamusonyeza chikondi chokhulupirika,Ngati mmene munalumbirira kwa makolo athu kalekale.+
72 Adzakwaniritsa zimene analonjeza makolo athu akale ndipo adzawasonyeza chifundo. Iye adzakumbukira pangano lake loyera,+ 73 lumbiro limene analumbira kwa kholo lathu Abulahamu,+
13 Pamene Mulungu analonjeza Abulahamu, analumbira pa dzina lake chifukwa panalibe wina wamkulu kuposa iyeyo amene akanamulumbirira.+ 14 Iye anati: “Ndithudi ndidzakudalitsa ndipo ndidzachulukitsa mbadwa zako.”+