-
Genesis 12:15, 16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Nawonso akalonga a Farao anamuona ndipo anakauza Farao kuti mkaziyo ndi wokongola. Choncho mkaziyo anatengedwa nʼkupita naye kunyumba kwa Farao. 16 Farao anamusamalira bwino Abulamu chifukwa cha mkazi wake, moti anamupatsa nkhosa, ngʼombe, abulu aamuna ndi aakazi, antchito aamuna ndi aakazi komanso ngamila.+
-