Tito 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zinthu zimenezi timakhala nazo chifukwa cha chiyembekezo cha moyo wosatha,+ chimene Mulungu amene sanganame+ analonjeza kalekale. Aheberi 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anachita zimenezo kuti pa zinthu ziwiri zosasinthika, zomwe chifukwa cha zimenezi nʼzosatheka kuti Mulungu aname,+ ife amene tathawira kumalo otetezeka tilimbikitsidwe nʼkumakhulupirira kwambiri* zinthu zimene tikuyembekezera.
2 Zinthu zimenezi timakhala nazo chifukwa cha chiyembekezo cha moyo wosatha,+ chimene Mulungu amene sanganame+ analonjeza kalekale.
18 Anachita zimenezo kuti pa zinthu ziwiri zosasinthika, zomwe chifukwa cha zimenezi nʼzosatheka kuti Mulungu aname,+ ife amene tathawira kumalo otetezeka tilimbikitsidwe nʼkumakhulupirira kwambiri* zinthu zimene tikuyembekezera.