Deuteronomo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Yehova anandiuza kuti, ‘Tsogolera anthuwa ndipo mukonzekere ulendo, kuti akalowe nʼkutenga dziko limene ndinalumbira kwa makolo awo kuti ndidzawapatsa.’+ Yoswa 21:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Palibe lonjezo* limene silinakwaniritsidwe, pa malonjezo onse abwino amene Yehova analonjeza nyumba ya Isiraeli. Onse anakwaniritsidwa.+
11 Kenako Yehova anandiuza kuti, ‘Tsogolera anthuwa ndipo mukonzekere ulendo, kuti akalowe nʼkutenga dziko limene ndinalumbira kwa makolo awo kuti ndidzawapatsa.’+
45 Palibe lonjezo* limene silinakwaniritsidwe, pa malonjezo onse abwino amene Yehova analonjeza nyumba ya Isiraeli. Onse anakwaniritsidwa.+