1 Mafumu 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ponena za nyumba ukumangayi, ukamatsatira malamulo anga ndiponso kusunga ziweruzo zanga zonse,+ inenso ndidzakwaniritsa zimene ndinalonjeza Davide bambo ako.+
12 “Ponena za nyumba ukumangayi, ukamatsatira malamulo anga ndiponso kusunga ziweruzo zanga zonse,+ inenso ndidzakwaniritsa zimene ndinalonjeza Davide bambo ako.+