Miyambo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mawu a munthu amene amalankhula asanaganize amalasa ngati lupanga,Koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+ Miyambo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mawu achilungamo amasangalatsa mafumu. Iwo amakonda munthu amene amalankhula moona mtima.+
18 Mawu a munthu amene amalankhula asanaganize amalasa ngati lupanga,Koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+