-
1 Mafumu 16:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mʼchaka cha 26 cha Asa mfumu ya Yuda, Ela mwana wa Basa anakhala mfumu ya Isiraeli ku Tiriza ndipo analamulira zaka ziwiri.
-
-
1 Mafumu 16:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma anthu amene ankatsatira Omuri anagonjetsa amene ankatsatira Tibini mwana wa Ginati. Choncho Tibini anafa ndipo Omuri anakhala mfumu.
-