Deuteronomo 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti anthu a Yehova ndi gawo lake.+Yakobo ndiye cholowa chake.+ Salimo 135:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ya wasankha Yakobo kuti akhale wake,Wasankha Isiraeli kuti akhale chuma chake chapadera.*+