-
Luka 17:1, 2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kenako Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Nʼzosatheka kuti pakhale popanda zopunthwitsa. Koma tsoka kwa munthu amene zopunthwitsazo zimadzera mwa iye! 2 Zingamukhalire bwino kwambiri atamumangirira chimwala cha mphero mʼkhosi mwake nʼkumuponya mʼnyanja, kusiyana ndi kuti akhumudwitse mmodzi wa tiana iti.+
-