Mateyu 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho omalizira adzakhala oyambirira ndipo oyambirira adzakhala omalizira.”+ Maliko 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma ambiri amene ali oyamba adzakhala omaliza ndipo omaliza adzakhala oyamba.”+ Luka 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndithudi amene ali omalizira adzakhala oyamba, ndipo oyamba adzakhala omalizira.”+