2 Mafumu 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Komabe mtundu uliwonse unapanga mulungu wake nʼkukamuika* mʼkachisi pamalo okwezeka amene Asamariya anamanga. Mtundu uliwonse unachita zimenezi mʼmizinda imene unkakhala. 2 Mafumu 17:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho ankaopa Yehova koma ankalambira milungu yawo, mogwirizana ndi chipembedzo cha mitundu imene anawatengako.+
29 Komabe mtundu uliwonse unapanga mulungu wake nʼkukamuika* mʼkachisi pamalo okwezeka amene Asamariya anamanga. Mtundu uliwonse unachita zimenezi mʼmizinda imene unkakhala.
33 Choncho ankaopa Yehova koma ankalambira milungu yawo, mogwirizana ndi chipembedzo cha mitundu imene anawatengako.+