-
Yohane 9:35-37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Yesu anamva kuti munthu uja amuchotsa musunagoge. Ndipo atakumana naye anamufunsa kuti: “Kodi ukukhulupirira Mwana wa munthu?” 36 Munthuyo anayankha kuti: “Kodi mwana wa munthuyo ndi ndani? Ndiuzeni bambo kuti ndimukhulupirire.” 37 Yesu anamuuza kuti: “Wamuona kale, ndipo ndi amene akulankhula nawe panopa.”
-