Levitiko 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Muzisunga malamulo anga ndi zigamulo zanga. Aliyense amene akuchita zimenezi adzakhala ndi moyo chifukwa cha malamulo ndi zigamulo zimenezo.+ Ine ndine Yehova. Agalatiya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Chilamulo sichidalira chikhulupiriro. Koma “aliyense amene akuchita za mʼChilamulo adzakhala ndi moyo chifukwa cha chilamulocho.”+
5 Muzisunga malamulo anga ndi zigamulo zanga. Aliyense amene akuchita zimenezi adzakhala ndi moyo chifukwa cha malamulo ndi zigamulo zimenezo.+ Ine ndine Yehova.
12 Tsopano Chilamulo sichidalira chikhulupiriro. Koma “aliyense amene akuchita za mʼChilamulo adzakhala ndi moyo chifukwa cha chilamulocho.”+