Yesaya 45:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndalumbira pa dzina langa.Mawu amene atuluka pakamwa panga ndi olondola,Ndipo adzakwaniritsidwa ndithu:+ Bondo lililonse lidzandigwadira,Ndipo lilime lililonse lidzalumbira kuti lidzakhala lokhulupirika kwa ine,+
23 Ndalumbira pa dzina langa.Mawu amene atuluka pakamwa panga ndi olondola,Ndipo adzakwaniritsidwa ndithu:+ Bondo lililonse lidzandigwadira,Ndipo lilime lililonse lidzalumbira kuti lidzakhala lokhulupirika kwa ine,+