2 Akorinto 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye watidinda chidindo chake.+ Chidindo chimenechi ndi mzimu woyera+ womwe uli mʼmitima mwathu ndipo uli ngati madalitso amʼtsogolo. Aefeso 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Komanso, musamamvetse chisoni mzimu woyera wa Mulungu,+ umene Mulunguyo anaugwiritsa ntchito pokuikani chidindo+ kuti mudzamasulidwe ndi dipo+ pa tsiku lachipulumutso. Chivumbulutso 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno ndinamva chiwerengero cha amene anadindidwa chidindo. Anthu okwana 144,000,+ ochokera mʼfuko lililonse la ana a Isiraeli, anadindidwa chidindo:+
22 Iye watidinda chidindo chake.+ Chidindo chimenechi ndi mzimu woyera+ womwe uli mʼmitima mwathu ndipo uli ngati madalitso amʼtsogolo.
30 Komanso, musamamvetse chisoni mzimu woyera wa Mulungu,+ umene Mulunguyo anaugwiritsa ntchito pokuikani chidindo+ kuti mudzamasulidwe ndi dipo+ pa tsiku lachipulumutso.
4 Ndiyeno ndinamva chiwerengero cha amene anadindidwa chidindo. Anthu okwana 144,000,+ ochokera mʼfuko lililonse la ana a Isiraeli, anadindidwa chidindo:+