Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 8:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho ngati tili ana, ndifenso olandira cholowa kuchokera kwa Mulungu. Koma ndifenso olandira cholowa+ anzake a Khristu, ngati tikuvutika naye limodzi+ kuti tikalandire naye ulemerero.+

  • Aefeso 1:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma inunso munakhala ndi chiyembekezo mwa iye mutamva mawu a choonadi, omwe ndi uthenga wabwino wonena za chipulumutso chanu. Mutakhulupirira, Mulungu anagwiritsa ntchito mzimu woyera umene analonjeza kuti akuikeni chidindo+ ndipo anagwiritsa ntchito Khristu kuti achite zimenezi. 14 Mzimu woyerawo uli ngati chikole chotsimikizira kuti tidzalandira zimene Mulungu watilonjeza.+ Mulungu anachita zimenezi nʼcholinga choti apereke dipo+ kuti anthu ake amasulidwe.+ Zimenezi zidzachititsa kuti atamandidwe komanso kupatsidwa ulemerero.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena