1 Akorinto 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma ngati munthu amene sali pabanja akulephera kudziletsa, ndipo wapitirira pachimake pa unyamata, ndi bwino kuti akwatire.+ Sakuchimwa. 1 Akorinto 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi tilibe ufulu woyenda limodzi ndi akazi athu okhulupirira+ ngati mmene amachitira atumwi ena onse, abale awo a Ambuye+ komanso Kefa?*+
36 Koma ngati munthu amene sali pabanja akulephera kudziletsa, ndipo wapitirira pachimake pa unyamata, ndi bwino kuti akwatire.+ Sakuchimwa.
5 Kodi tilibe ufulu woyenda limodzi ndi akazi athu okhulupirira+ ngati mmene amachitira atumwi ena onse, abale awo a Ambuye+ komanso Kefa?*+