Deuteronomo 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndinachita mantha chifukwa cha mkwiyo waukulu umene Yehova anali nawo pa inu,+ moti ankafuna kukuwonongani. Koma pa nthawi imeneyinso Yehova anandimvetsera.+
19 Ndinachita mantha chifukwa cha mkwiyo waukulu umene Yehova anali nawo pa inu,+ moti ankafuna kukuwonongani. Koma pa nthawi imeneyinso Yehova anandimvetsera.+