2 Petulo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipotu Mulungu sanalekerere angelo amene anachimwa aja+ osawapatsa chilango. Koma anawaponya mu Tatalasi,*+ anawamanga mumdima wandiweyani podikira kuti adzawaweruze.+ Yuda 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiponso angelo amene anasiya utumiki umene Mulungu anawapatsa kumwamba komanso malo amene ankayenera kukhala,+ Mulungu anawamanga ndi maunyolo omwe sangaduke* nʼkuwasunga mumdima wandiweyani kuti adzaweruzidwe pa tsiku lalikulu.+
4 Ndipotu Mulungu sanalekerere angelo amene anachimwa aja+ osawapatsa chilango. Koma anawaponya mu Tatalasi,*+ anawamanga mumdima wandiweyani podikira kuti adzawaweruze.+
6 Ndiponso angelo amene anasiya utumiki umene Mulungu anawapatsa kumwamba komanso malo amene ankayenera kukhala,+ Mulungu anawamanga ndi maunyolo omwe sangaduke* nʼkuwasunga mumdima wandiweyani kuti adzaweruzidwe pa tsiku lalikulu.+