Yoswa 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Malirewo anabwerera ku Rama, mpaka kukafika kumzinda wa Turo+ wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri. Kenako anabwereranso ku Hosa nʼkukathera kunyanja mʼchigawo cha Akizibu.
29 Malirewo anabwerera ku Rama, mpaka kukafika kumzinda wa Turo+ wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri. Kenako anabwereranso ku Hosa nʼkukathera kunyanja mʼchigawo cha Akizibu.