-
2 Mbiri 34:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Anthuwo anali kugwira ntchitoyo mokhulupirika.+ Atsogoleri awo oti aziwayang’anira anali Yahati ndi Obadiya, omwe anali Alevi ochokera mwa ana a Merari,+ ndiponso Zekariya ndi Mesulamu ochokera mwa ana a Akohati.+ Aleviwo, amene aliyense wa iwo anali katswiri wodziwa kuimba ndi zipangizo zoimbira,+
-