Yesaya 54:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kulitsa hema wako.+ Nsalu za hema wako wamkulu zitambasulidwe. Usaumire pochita zimenezi. Talikitsa zingwe za hema wako ndipo ulimbitse zikhomo zake.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:2 Yesaya 2, ptsa. 221-222 Nsanja ya Olonda,1/1/1995, tsa. 16
2 “Kulitsa hema wako.+ Nsalu za hema wako wamkulu zitambasulidwe. Usaumire pochita zimenezi. Talikitsa zingwe za hema wako ndipo ulimbitse zikhomo zake.+