Maliko 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kumeneko khamu la anthu linasonkhananso, mwakuti sanathe n’komwe kudya chakudya.+