Luka 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano anthu okwana 70 aja anabwerera ali osangalala. Iwo anauza Yesu kuti: “Ambuye, ngakhale ziwanda zinatigonjera+ pamene tinagwiritsa ntchito dzina lanu.” Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:17 Nsanja ya Olonda,7/1/1988, tsa. 17
17 Tsopano anthu okwana 70 aja anabwerera ali osangalala. Iwo anauza Yesu kuti: “Ambuye, ngakhale ziwanda zinatigonjera+ pamene tinagwiritsa ntchito dzina lanu.”