Luka 22:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Koma Petulo anati: “Munthu iwe, ine sindikudziwa zimene ukunena.” Nthawi yomweyo, mawu ali m’kamwa, tambala analira.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:60 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 8
60 Koma Petulo anati: “Munthu iwe, ine sindikudziwa zimene ukunena.” Nthawi yomweyo, mawu ali m’kamwa, tambala analira.+