Yohane 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Poyankha Yesu anauza mayiyo kuti: “Mukanadziwa mphatso+ yaulere ya Mulungu ndi amene+ akukuuzani kuti, ‘Mundipatseko madzi akumwa,’ mukanam’pempha iyeyo, ndipo akanakupatsani madzi amoyo.”+
10 Poyankha Yesu anauza mayiyo kuti: “Mukanadziwa mphatso+ yaulere ya Mulungu ndi amene+ akukuuzani kuti, ‘Mundipatseko madzi akumwa,’ mukanam’pempha iyeyo, ndipo akanakupatsani madzi amoyo.”+