Yohane 4:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pamenepo Asamariya ambiri ochokera mumzindawo anakhulupirira+ mwa iye chifukwa cha mawu a mayi uja amene pochitira umboni anati: “Iyeyu anandiuza zinthu zonse zimene ndakhala ndikuchita.”+
39 Pamenepo Asamariya ambiri ochokera mumzindawo anakhulupirira+ mwa iye chifukwa cha mawu a mayi uja amene pochitira umboni anati: “Iyeyu anandiuza zinthu zonse zimene ndakhala ndikuchita.”+