-
Yohane 7:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Pakuti palibe amene amachita kanthu mseri koma n’kumafuna kudziwika ndi anthu. Ngati inu mumachita zimenezi, mudzionetsere poyera kudzikoli.”
-