Yohane 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Yesu anati: “Nthawi yanga yoyenera sinakwanebe,+ koma kwa inu, iliyonse ndi nthawi yanu yoyenera.
6 Chotero Yesu anati: “Nthawi yanga yoyenera sinakwanebe,+ koma kwa inu, iliyonse ndi nthawi yanu yoyenera.