Yohane 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo tsopano Atate, ndiloleni kuti ndikhale pambali panu, ndipo mundipatse ulemerero umene ndinali nawo pambali panu dziko lisanakhalepo.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:5 Yesu—Ndi Njira, tsa. 280 Nsanja ya Olonda,10/15/2013, tsa. 279/15/1990, tsa. 8
5 Ndipo tsopano Atate, ndiloleni kuti ndikhale pambali panu, ndipo mundipatse ulemerero umene ndinali nawo pambali panu dziko lisanakhalepo.+