Yohane 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Komanso, ine sindikhalanso m’dzikoli pakuti ndikubwera kwa inu, koma iwo adakali m’dzikoli.+ Atate Woyera, ayang’anireni+ chifukwa cha dzina lanu limene mwandipatsa, kuti akhale amodzi mmene ife tilili.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:11 Yandikirani, tsa. 110
11 “Komanso, ine sindikhalanso m’dzikoli pakuti ndikubwera kwa inu, koma iwo adakali m’dzikoli.+ Atate Woyera, ayang’anireni+ chifukwa cha dzina lanu limene mwandipatsa, kuti akhale amodzi mmene ife tilili.+