Aroma 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo musapereke ziwalo zanu ku uchimo+ kuti zikhale zida zochitira zinthu zosalungama,+ koma dziperekeni kwa Mulungu monga anthu amene auka kwa akufa.+ Ziwalo zanunso muzipereke kwa Mulungu monga zida+ zochitira chilungamo. Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:13 ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, ptsa. 64-65
13 Ndipo musapereke ziwalo zanu ku uchimo+ kuti zikhale zida zochitira zinthu zosalungama,+ koma dziperekeni kwa Mulungu monga anthu amene auka kwa akufa.+ Ziwalo zanunso muzipereke kwa Mulungu monga zida+ zochitira chilungamo.