-
Aroma 16:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Moni kwa Turufena ndi Turufosa, akazi ogwira ntchito mwakhama potumikira Ambuye. Moni kwa Peresida, wokondedwa wathu. Mayi ameneyu wachita ntchito zambiri potumikira Ambuye.
-