-
1 Akorinto 7:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 ndipo amene akulira azikhala ngati amene sakulira. Amene akusangalala azikhala ngati amene sakusangalala, ndipo amene amagula zinthu azikhala ngati opanda kanthu.
-