2 Akorinto 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti ngati tinachita misala,+ tinachitira Mulungu. Ngati tili olongosoka,+ cholinga ndi kupindulitsa inuyo. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:13 Nsanja ya Olonda,12/15/1998, tsa. 16
13 Pakuti ngati tinachita misala,+ tinachitira Mulungu. Ngati tili olongosoka,+ cholinga ndi kupindulitsa inuyo.