1 Timoteyo 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Momwemonso, ntchito zabwino zimaonekera poyera,+ ndipo ngakhale kuti zisaonekere sizingabisike mpaka kalekale.+
25 Momwemonso, ntchito zabwino zimaonekera poyera,+ ndipo ngakhale kuti zisaonekere sizingabisike mpaka kalekale.+