1 Petulo 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pajatu mukudziwa kuti sizinali zinthu zotha kuvunda,+ siliva kapena golide, zimene zinakumasulani+ ku khalidwe lanu lopanda phindu limene munalilandira kuchokera kwa makolo anu mwa chikhalidwe chanu.
18 Pajatu mukudziwa kuti sizinali zinthu zotha kuvunda,+ siliva kapena golide, zimene zinakumasulani+ ku khalidwe lanu lopanda phindu limene munalilandira kuchokera kwa makolo anu mwa chikhalidwe chanu.