Chivumbulutso 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zimenezi zitatha, nditayang’ana ndinaona khomo lotseguka kumwamba. Ndipo mawu oyamba amene ndinawamva akundilankhula anali ngati kulira kwa lipenga.+ Mawuwo anali akuti: “Kwera kumwamba kuno,+ ndikuonetse zinthu zimene ziyenera kuchitika.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 74
4 Zimenezi zitatha, nditayang’ana ndinaona khomo lotseguka kumwamba. Ndipo mawu oyamba amene ndinawamva akundilankhula anali ngati kulira kwa lipenga.+ Mawuwo anali akuti: “Kwera kumwamba kuno,+ ndikuonetse zinthu zimene ziyenera kuchitika.”+