December Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya December 2018 Zimene Tinganene December 3-9 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 9-11 Munthu Amene Ankazunza Akhristu Anakhala Mkhristu Wakhama December 10-16 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 12-14 Baranaba ndi Paulo Ankathandiza Anthu Kukhala Ophunzira M’madera Akutali Kwambiri MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Muzithandiza Anthu Amene Ali ndi “Maganizo Abwino” Kuti Akhale Ophunzira December 17-23 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 15-16 Anasankha Zochita Pogwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tizitamanda Yehova Mosangalala Poimba Nyimbo December 24-30 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 17-18 Muzitsanzira Mtumwi Paulo pa Nkhani Yolalikira Komanso Kuphunzitsa December 31–January 6 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 19-20 “Mukhale Tcheru ndi Kuyang’anira Gulu Lonse la Nkhosa”