-
Kodi Maulosi Onena za Mesiya Amatsimikizira Kuti Yesu Analidi Mesiya?Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
-
-
Mthenga adzatsogola kudzalengeza za iye
-
-
Kodi Yohane M’batizi Anali Ndani?Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
-
-
Ntchito yake inanenedweratu: Pogwira ntchito yolalikira, Yohane anakwaniritsa ulosi wonena za mthenga wa Yehova. (Malaki 3:1; Mateyu 3:1-3) Iye anakwaniritsa udindo ‘wosonkhanitsira Yehova anthu okonzedwa,’ chifukwa anakonzekeretsa Ayuda anzake kuti alandire Yesu Khristu, yemwe ndi munthu amene anaimira Yehova Mulungu kuposa wina aliyense..—Luka 1:17.
-