Kodi Dziko Lapansi Lidzapulumuka?—Zifukwa Zokhalila na Ciyembekezo
Na. 1 2023
© 2023 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini ino si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika pa dziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa mwa zopeleka zaufulu. Kuti mucite copeleka, pitani pa donate.jw.org. Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kusiyapo ngati taonetsa ina.