Peji ya Mutu wa Buku/Peji ya Ofalitsa
Mvetselani kwa Mulungu
Kabuku aka si kogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza panchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imenei.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Koma tasintha masipeling’i kuti agwilizane ndi Cinyanja cimene talemba.
Kupulinta kwa mu 2011
Cinyanja (ld-CIN)
© 2011
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA