Peji ya Mutu wa Buku/Peji ya Ofalitsa
Ndani Amene Akucita Cifunilo Ca Yehova Masiku Ano?
Kabuku aka si kogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi.
Kuti mucite copeleka, pitani pa webusaiti ya www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Koma masipeling’i a Cinyanja m’kabuku kano tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
Ndani Amene Akucita Cifunilo ca Yehova Masiku Ano?
Who Are Doing Jehovah’s Will Today?
Kupulinta kwa mu November 2016
Cinyanja (jl-CIN)
© 2012, 2016 WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA