Peji ya Mutu wa Buku/Peji ya Ofalitsa
Kusanthula Malemba Tsiku na Tsiku—2023
Lemba la Caka “Mawu anu onse ndi coonadi cokha-cokha.”—Salimo 119:160.
Kabuku kano si kogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene ikucitika padziko lonse lapansi. Nchito imeneyi timaiyendetsa na zopeleka zaufulu.
Kuti mupange copeleka, pitani pa donate.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika, kusiyapo ngati taonetsa ina. Komabe, ena mwa masipeling’i a Cinyanja m’kabuku kano tatsatila malamulo a m’buku lakuti A Unified Standard Orthography for South-Central African Languages.
Kanapulintiwa mu June 2022
Cinyanja (es23-CIN)
© 2022
WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA