Zamkati
August 1, 2013
Kodi Zamalisece—Zilibe Vuto?
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. All rights reserved.
NKHANI ZOPHUNZILA
SEPTEMBER 30, 2013–OCTOBER 6, 2013 | TSAMBA 8 • NYIMBO: 125, 66
Monga atumiki odzipeleka a Yehova, tapatulidwa kuti ticite utumiki wopatulika. M’nkhani ino, tidzapenda lemba la Nehemiya caputala 13. Tidzakambilana mfundo zinai zimene zingatithandize kuti tikhalebe oyela mwa kuuzimu.
OCTOBER 7-13, 2013 | TSAMBA 13 • NYIMBO: 119, 80
M’nkhani iyi tidzapenda zinthu zisanu zimene zingapangitse Mkristu wokhulupilika ‘kukwiila Yehova.’ (Miy. 19:3) Kenako tidzakambilana mozama njila zisanu zimene zingatithandize kupewelatu kuimba mlandu Yehova cifukwa ca mavuto athu.
OCTOBER 14-20, 2013 | TSAMBA 18 • NYIMBO: 124, 20
Ganizilanani ndi Kulimbikitsana
OCTOBER 21-27, 2013 | TSAMBA 23 • NYIMBO: 61, 43
Ganizilani za Mtundu wa Munthu Amene Muyenela Kukhala
Pa nkhani ziŵilizi, yoyamba ifotokoza zimene tiyenela kucita kuti tithandizane kukhalabe olimba mosasamala kanthu za mavuto amene tingakumane nao. Nkhani yaciŵili idzafotokoza zimene tingacite kuti tigonjetse ziyeso zimene Satana amagwilitsila nchito pofuna kuononga ubwenzi wathu ndi Mulungu.
NKHANI ZINA M’MAGAZINI INO
Kodi Zamalisece Zilibe Vuto? 3
Tsanzilani Cikhulupililo Cao—Anam’sunga“Pomupulumutsa Pamodzi ndi Anthu Ena 7” 28