LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp16 na. 4 tsa. 1
  • Baibulo—Mmene Yapulumukila

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Baibulo—Mmene Yapulumukila
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2016
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2016
wp16 na. 4 tsa. 1
Magazini ya Nsanja ya Mlonda ya, Na. 4 2016 | Baibulo—Mmene Yapulumukila

Baibulo—Mmene Yapulumukila

Na. 4 2016

© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania

MAGAZINI ya Nsanja ya Mlonda, imalemekeza Yehova Mulungu, amene ndi Wolamulila wa cilengedwe conse. Imalimbikitsa anthu ndi uthenga wabwino wakuti posacedwa, Ufumu wa Mulungu udzacotsa zoipa zonse ndi kusintha dziko lapansi kukhala paradaiso. Imalimbikitsa anthu kukhulupilila Yesu Khiristu amene anatifela kuti tikapeze moyo wosatha, ndipo panthawi ino iye akulamulila monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Magaziniyi yakhala ikufalitsidwa kuyambila mu 1879 ndipo si yandale. Mfundo zake zonse n’zocokela m’Baibulo.

Magazini iyi si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibulo imene imacitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi.

Kuti mucite copeleka, pitani pa webusati ya www.jw.org.

Baibulo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kusiyapo ngati taonetsa ina.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani