Mungacite Ciani Kuti Mupindule na Zimene Muŵelenga m’Baibo?
Na. 1 2017
© 2016 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
Magazini iyi si yogulitsa. Colinga cake ni kuthandiza pa nchito yophunzitsa Baibo imene imacitika padziko lonse lapansi. Zopeleka zaufulu n’zimene zimathandiza kupititsa patsogolo nchito imeneyi.
Kuti mucite copeleka, pitani pa webusaiti ya www.jw.org.
Baibo imene taseŵenzetsa ni Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika kusiyapo ngati taonetsa ina.
MAGAZINI ya Nsanja ya Mlonda, imalemekeza Yehova Mulungu, amene ndi Wolamulila wa cilengedwe conse. Imalimbikitsa anthu ndi uthenga wabwino wakuti posacedwa, Ufumu wa Mulungu udzacotsa zoipa zonse ndi kusintha dziko lapansi kukhala paradaiso. Imalimbikitsa anthu kukhulupilila Yesu Khiristu amene anatifela kuti tikapeze moyo wosatha, ndipo panthawi ino iye akulamulila monga Mfumu ya Ufumu wa Mulungu. Magaziniyi yakhala ikufalitsidwa kuyambila mu 1879 ndipo si yandale. Mfundo zake zonse n’zocokela m’Baibo.